Chitowo Medical Private Clinic

Chitowo Medical Private Clinic The offered services include: Out Patient Department ( OPD ), HIV Testing & Counselling, Family Planning methods, Under Five Services E.g Weighing

 Wapolisi yemwe amagwira ntchito m'boma la  Dedza a Eric Chasweka wadzipha podzimangilira m'nyumba yake.Mneneri wa apoli...
03/06/2025


Wapolisi yemwe amagwira ntchito m'boma la Dedza a Eric Chasweka wadzipha podzimangilira m'nyumba yake.

Mneneri wa apolisi m'chigawo chapakati chakuzambwe, a Foster Benjamin watsimikiza za nkhaniyi kuti a Chasweka anafika ku ntchito komaliza lachisanu ndipo ataweruka sanabwelerenso m'masiku otsatira.

A Benjamin ati izi zinachitsa kuti apolisi anzawo apite kunyumba yake komwe anathyola chitseko chanyumbayi.

Iwo ati anapezaso kalata zauthenga otsanzika kwa mkulu wa polisi ya Dedza, makolo ake komanso bwenzi lake.

Kumadyatu zamafuta kumeneko. Mwakakumbuka kameneka?
03/06/2025

Kumadyatu zamafuta kumeneko. Mwakakumbuka kameneka?

06/05/2023

CURRENT SERVICES OFFERED BY CHITOWO MEDICAL PVT CLINIC. HIV TESTING SERVICES, FAMILY PLANNING, OUTPATIENT, UNDER 5 WEIGHING SERVICE ETC

24/08/2022

Address

Chitowo Trading Centre. Post Office Box 136
Dedza

Telephone

+265997418381

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chitowo Medical Private Clinic posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Chitowo Medical Private Clinic:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram