Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Fighting Against Hiv/Aids and Sti PHUNZILANI ZA HIV/AIDS NDIMATENDA OPATSILANA POGONANA MULI KUNYUMBA. UTHENGA WA CHIPATALA.PANGANI FOLLOW PAGE LATHU.
*ART AND STI CLINICAL MENTOR*
(1)

Bambo mbu mwana mbuuu. Exactly zonse mumapezeka mulibe ku chipatala and blame imabwera kwa inu kuti mkugulisa mankhwala ...
12/03/2026

Bambo mbu mwana mbuuu.
Exactly zonse mumapezeka mulibe ku chipatala and blame imabwera kwa inu kuti mkugulisa mankhwala pamene kumakhala kulibe ndithu. Koma ma ARV samatha always in stock. Andale nthawi zonse akuuzani kuti mankhwala aliko. Nde ngati aliko chifukwa chani sapitako akadwala????

pepani mumva ngati mkutitsiya so basi ziiiiiii
12/03/2026

pepani mumva ngati mkutitsiya so basi ziiiiiii

kodi ndinu HIV mumayezera maso aja?munthu akakhala owonda basi alindi  HIV. anenepa basi amuyanja ma ARV.ana anjoka
12/03/2026

kodi ndinu HIV mumayezera maso aja?
munthu akakhala owonda basi alindi HIV. anenepa basi amuyanja ma ARV.
ana anjoka

12/03/2026

kulibe mawu oti ine ndi carrier wa HIV.
ukapezeka negative ndekuti ulibe komaso sungapelekeso kwa wina

12/03/2026

Good morning team
imagine mnthu wamuna kukamudula mbokoshen chifukwa chamatenda opatsilana pogonana

incase simunaonepo chinthu chabwino lero.here I come
11/03/2026

incase simunaonepo chinthu chabwino lero.
here I come

11/03/2026

Lucia Kaomba Kazembe writes:

Let’s clear the air!!! Lots of questions about
Why surgeries get cancelled? (The Truth About the "Waiting List")

We’ve all heard the stories: You prepare for surgery, you fast, you get to the hospital, and then—at the last minute—you are told to go home and come back in three months.

The common myth is that doctors cancel surgeries to force patients into their private clinics for money. But as someone at Queen Elizabeth Central Hospital (QECH), I want to share the reality of what actually happens behind those theater doors.

1. The "Emergency Leapfrog" 🚑
At Queens, we do not have a dedicated theater just for emergencies. If a victim of a road accident comes and needs an emergency operation they will be rushed in, they cannot wait. To save a life right now, we have to stop the "elective" (planned) list.
Your surgery isn't cancelled because we don't care; it’s cancelled because someone else is about to die if they don’t get operated within an hour or 2.

2. Resource constraints: some operations require skills that only one or two surgeons posses in the department. If that surgeon is away, the other more junior surgeons cannot proceed without oversight.

Some operations require admission to the intensive care unit after the operation. QECH only has 7 ICU beds, if the night before your operation an emergency occurred and a patient was admitted on the bed booked for you, we have to cancel.

Anaesthesia!!! Akulu akulu, pain has to be eliminated for a successful operation. We cannot be operating while you scream in pain. If we do not have an anaesthetist (because the numbers are lacking) allocated to our theatre, the list will be canceled.

3.The Booking "Train" Never Stops 🗓️
Think of the surgical list like a train that is always moving.
On Monday, we see patients in the clinic and book them for the next available dates.
On Tuesday, we see more patients and fill the next gaps.
This happens every single day.
If your surgery is cancel

11/03/2026

azibambo akulu akulu a ndalama zawo ndi maphunziro abwino ndamene akugawa ndalama komaso matenda kwa atsikana achichepele. wina ukuti wapeza size yako osaziwa kuti ndi size ya bamboo ako.

11/03/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chikondi Onion, Charity Agness Chitanda, Hosseah Maganizo, Leila Abdalla, Waseem Abbas Rind, Richard Banda, Clement Tabu, Walter Phiri Junior, Mahirasi Malunga, Mwaii Fenias, Lonjez Grant, Yanakiss Nation, Joe Mtsu, Midæ Bêib, Dimension Kingkhadesh, Dolicah Muyeni, Lexon Moses, Mike Sumani, Elizabeth Wa Masiku, Jazzi Baogalafi

11/03/2026

koma mkuziwa kuti anthu ozindikila ndamene amatenga matenda mophweka ?

11/03/2026

MBULI ZOPHUNZIRA KUKANA KUMWA MA ARV.
AMENE MUMAWADALILA KUTI NDI OPHUNZILAWA KUPHATIKIZAPO ENA AKU CHIPATALA AKUCHITISA MANYAZIII. ZIKAWAPETA NDIPAMENE AMATHAN
MANGIRA ATI TIMAKAIKILA NGATI NDIZOONA. KOMA ZOONAAAAAAAA

Munthu ndiwe wa chipatala bwino bwino, ukuziwa ubwino wama ARV ndi kuipa kwa HIV koma akusiyaso kumwa mankhwala etiiii, ...
11/03/2026

Munthu ndiwe wa chipatala bwino bwino, ukuziwa ubwino wama ARV ndi kuipa kwa HIV koma akusiyaso kumwa mankhwala etiiii, ena akukana kuyamba kumwa mankhwala. Zinthu zake zovuta etiii.

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fighting Against Hiv/Aids and Sti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Fighting Against Hiv/Aids and Sti:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram