Ralph's herbalist

Ralph's herbalist Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ralph's herbalist, Medical and health, Ndilande sda main church, Blantyre.

11/02/2022

ameretsa msipu ziudye ng'ombe ndi tsamba achite nazo munthu, atulutse chakudya chochokera mthaka ( plsm 104 v14) mulungu wathu ndi mulungu wa order anaika chilichonse mmalo mwache Ndikuti chigwire ntchito yake moyenera verse lo likuti ndizitsamba achitezo Munthu which means ifeyo kuti tipeze machilitso we need kugwilitsa ntchito chilengedwe muchingelezi zimemvekako bwino( herbs for the service fo man) zomwe zikuonetseratu kuti ifeyo tikiyenera kupanga depend on it, kuti tipeze relief kumatenda athu. Ndiye verse lo kumatepoko likuti anatulutse chakudya chochokera mthaka. Kodi pamene akufuna tiuzenji? Mene thupi lathuli linapangidwira ilikuyenera kulandira chakudya chomwe chili chofunika not kumangodya zili zonse ndizosadya zomwe ayi chakudya chochokera mthaka which mean zomera komaso zomwe zili organic not zothira mankhwala ndi fertilizer ayi ndichifukwa chake masiku ano tikudwala Matenda Monga bp diabetes, stroke Cancer kungochulapo yochepa chabe. Koma gwero la zonsezi ndi kudya ( eat) tisaiwale kuti munthu anachimwa chifukwa cha food ngati anthu tikufa ( death) nkhani yake ndi zakudya, ndiye pa death mukachotsapo D ali koyambilirayo ndikuchotsaponso H wakumapetoyo mupeza kuti nkhani ndi eat. Ndichomwe chikutipha anthufe. Hosea 4 v 6 mulungu akudalitseni mukhale ndi mmawa wopambana

Address

Ndilande Sda Main Church
Blantyre
1704

Opening Hours

09:00 - 17:00

Telephone

+265888987660

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ralph's herbalist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram