Health & Healing Herbs

Health & Healing Herbs Moyo wathanzi muchilengedwe

22/10/2025

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Budo Akobrah Junioh Biwi, Moosa Argentina, Nafe Sanudi, Stagger Sisha, Fredoh Kamzy, Gift Darbs, Daniel Robert, Mpoto mpoto, Benjamin Chinguwo

16/10/2025

😂😂😂🤣🤣🤣Apa sizinayende😂🤣

12/10/2025

MTAMBIRA MMADZI (PARSLAIN)
✓Bwerani pano ma vegetarians ndi ma vegans ticheze pang'ono. Komabe ali yense asendere kuno ticheze nkhani yabwino yokhudzana ndi mtambira mmadzi kapena kuti parslain.
✓Ichi ndi chomera chomwe chimayanga pansi ndipo chimamera pamalo pomwe pali madzi okwanira. Chimapezeka kwambiri dzinja. Ndiye dzinja layandikira zedi ndipo tikuyenera kuphunziriratu za chomera chimenechi.
✓Ku France amalima ndipo amamukonda zedi.
✓Amadyedwa monga ndiwo. Mukhoza kuphika payekha ndi kutsira nsinjiro, kapena kusakaniza ndi bonongwe, nkhwani, komanso chisoso.
✓Mukhoza kupanga juice wa mtambira mmadzi ndi kumwa tambula imodzi patsiku.
✓Koma lero tikambirane za mtambira mmadzi ndi Omega-3 fatty acids.
✓Mtambira mmadzi ndi chomera chokhacho chomwe chiri ndi mlingo waukuru wa Omega-3 fatty acids. Chikupambana Chia seeds, flax seeds, nthanga za maungu ndi zomera zina zonse.
✓Mwanjira yanji? Omega-3 fatty acids alipo wa mitundu iwiri. ALA ndi EPA. ALA amapezeka mu zomera pomwe EPA amapezeka mu zamoyo monga nyama ndi nsomba. Ndiye amatitu nsomba ndi yomwe ili ndi Omega-3 fatty acids ochuruka, makamaka mutu wake. Tiime pang'ono apa. Nsomba ili ndi mtundu wa Omega-3 fatty acids wotchedwa kuti EPA osati ALA. Ndiye kuti ma vegans ndi ma vegetarians sapeza EPA.
✓Koma chinthu chimodzi chokondweretsa ndi choti mtambira mmadzi ali ndi mitundu yonse ya Omega-3 fatty acids. Choncho kudya mtambira mmadzi ndikofunikira zedi pa nkhani ya omega 3 fatty acids.

Ndiyimire kaye pomwepa. Usiku wabwino ma vegetarians nonse!

07/12/2024

*KUCHULUSA UMUNA*

_Simple way yosavuta njira iyi_

```Inu munayambapo mwakomora mkazi️ ndi kuchuluka Kwa umuna??```

*Mwamuna weniweni azikoza zozaza basen🛢️ osati tamukapu ayi*

Sakanizani izi

_Pezani mapira🌾 mpunga ovuika, gondolosi, ndi janus, chinangwa, ndi zamukati mwa coconut milk_ ,,kumapeto kwakeko muzatafune matowo awiri,

Uviikeni mpunga uja sukani katondo kanu thirani zose zija zisinjeni nde muzathiremo 1 teaspoon ya sugar nde muzidya ngati chiponde, Kaya muthiramo timazi wezi nde muzichita kumwa,,,, aaaaaaaa basi inuyo muzakhala akamuna,,,,,,, kukuza ngati mukuthirila mbeu🚿. Siku limenero nangati sanakomokepo muzandiuza,, kuti athamandngira nawo ku hospital
😋😋😋😋

ANTHU MUPHANA🤣🤣
17/11/2024

ANTHU MUPHANA🤣🤣

12/11/2024

Amene comment yake sikhala ndi like Pali Ka mofaya Ka week apa let's Go 😂😭

11/11/2024

Ngatisiwe nkhalamba
Palima 8 angati apa
&&&&&&&&&&&&&&8
&&&&8&&&&&&&&&&
50 marks

11/11/2024

Wamisala wina mu limbe anat lelo likadakhala dzuro bwez mawa Lili lachsanu, kod wamisalayu adayankhura lachngat??? 5pn ilipo

10/11/2024

Tione mbuli apa
I...........to school today.

(Went/go/gose/the)

10/11/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Louriam Benhayon, Mbulaheni Elsie, Elvis Katontoka, Dili Dilihani Nadeesha

*YONI DETOX PEARLS NDICHANI?*Awa ndimankhwala achilengedwe opangidwa kuchokela ku zisamba omwe amathana ndimavuto aliwon...
09/10/2024

*YONI DETOX PEARLS NDICHANI?*
Awa ndimankhwala achilengedwe opangidwa kuchokela ku zisamba omwe amathana ndimavuto aliwonse okhuza njira ya Chibelekero cha amayi (Gynecological problems) ndipo ena mwa mavuto omwe Yoni Detox Pearls amathana nawo ndi;

1.zotupa zamuchiberekero

2.kukanika kutenga pakati

3.akatenga pakati pakumachoka

4.mauka

5.kutulutsa chikazi chotsakhala bwino chonunkha

6. fungo lakundata

7. kukula kwa ndata

8 nthenda ya munjira yamkozo/ UTI

9. kusekeka kwa chibelekero

10. endometriosis

11.ululu pogona ndi mwamuna

12.ululu nthawi yosamba (cramps)

13. kusamba kosaleka

14 komanso kusasamba kumene.

*Mk4, 000 only*

Yoni detox pearls amayamwa zonyasa zonse zamuchiberekero komanso kundata kuzitulutsa kunja, kuphwetsa zotupa zonse, zoonongeka zonse kuzikonza mpaka mafungo onse kutha mayi kukhala ndi muchiberekero mokonzeka bwino kutenga pakati mbali inayi ndata kuisiya yochepa yothina bwino.

Call/WhatsApp 0882898854

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Health & Healing Herbs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram