Care MW

Care MW careMW󱢏
"Timaphunzitsa kapewedwe ka matenda osiyanasiyana.
(3)

Mwaulele,muli kunyumba kwanu"
" ONCE YOU SEE THIS FOLLOW THE PAGE"
"INVANI ZOONA ZOKHUZA KUCHIPATALA "
"KUCHIMAKE KWA UPHUNGU WAKUCHIPATALA "
👉caremw217@gmail.com.WhatsAp0999376652

06/03/2026

Kwabwela chenjezo kwa madokotala onse 🥹

゚viralシfypシ゚ ゚viralシfypシ゚viralシalシ

06/03/2026

"If you’re happy, if you’re feeling good, then nothing else matters." - Good morning 🌄

komatu team chipatala tanyozeka kayankhulidwe kabwanj aka 🥹?
05/03/2026

komatu team chipatala tanyozeka kayankhulidwe kabwanj aka 🥹?

ambiri akungodikila advert yolemba ntchito anthu kuchipatala sinanga ndi ena mwa Malo a essential komanso a critical 🫡
05/03/2026

ambiri akungodikila advert yolemba ntchito anthu kuchipatala sinanga ndi ena mwa Malo a essential komanso a critical 🫡

Diphallia.ndi pamene mwana wabadwa ndi zida(pen*s) ziwili komabe mukupita kwa nthawi mothandizidwa ndi achipatala imodzi...
05/03/2026

Diphallia.ndi pamene mwana wabadwa ndi zida(pen*s) ziwili komabe mukupita kwa nthawi mothandizidwa ndi achipatala imodzi imafota🫡

nawotu Azibale athu anati tiyime Kaye ndijambuliseko ndanyamata azigubuwa 😆, Good morning team chipatala 🌄
05/03/2026

nawotu Azibale athu anati tiyime Kaye ndijambuliseko ndanyamata azigubuwa 😆, Good morning team chipatala 🌄

very bad news njex 🥹💔 atakhala kuchipatala ku mzuzu central hospital kwakanthawi modzi mwa anthu oziwika bwino pa nkhani...
04/03/2026

very bad news njex 🥹💔 atakhala kuchipatala ku mzuzu central hospital kwakanthawi modzi mwa anthu oziwika bwino pa nkhani zoyimba nyimbo zachitonga watisiye Lero pepan nonse ananfedwa😭

Kodi mwati kuli ma interview achan 🥹 za HSA sizinatuluketu 😱
04/03/2026

Kodi mwati kuli ma interview achan 🥹 za HSA sizinatuluketu 😱

Goodmorning team chipatala.
04/03/2026

Goodmorning team chipatala.

04/03/2026

🚨🚨THE GOAL, IS DO IT 21 TIMES PER MONTH, TO PREVENT PROSTATE CANCER 🙌OSAMAYIWARA

Munthu modzi, mwa anthu 23 ena ali onse, ali ndi kachilombo (HIV) koyambitsa matenda a AIDS kuno ku Malawi. Kutengera zo...
03/03/2026

Munthu modzi, mwa anthu 23 ena ali onse, ali ndi kachilombo (HIV) koyambitsa matenda a AIDS kuno ku Malawi.

Kutengera zomwe Bungwe la National Auds Commission lapeza, vuto li ndil la likulu ku Blantyre City, pa number 2 Pali Lilongwe City, pa number 3 Mulanje, namba 4 Mangochi ndipo Thyolo ndi yomwe amangilira top 5

Top 5, ku maboma aku mwera mpaka maboma 4, muchepetse ma plain kumeneko.

03/03/2026

pa post iyi tikufunila zabwino kwa onse omwe akufuna atenge mimba chaka chino 🤲

Address

Area
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Care MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Care MW:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram