29/11/2025
As the month of November comes to an end, Umoyo N'kukambirana shifts its focus from Antimicrobial Resistance discussions to discuss about World AIDS Day falling on 1st December, where we will explore this yearโs theme, " We Remember, We Lead, We Rise to Transform the Response".
Our guests from the Blantyre District Health Office, Blantyre District Council and National Aids commission will join us in the program to unpack facts about this topic.
Tune in to Times Radio from 5:00 PM to 6:00 PM to be part of this meaningful discussion.
.......................................................................................
Mu mwezi wa November, mu pulogalamu ya Umoyo N'kukambirana takhala tikufotokoza za kupima Kwa tizilombo toyambitsa matenda ku mankhwala.
Pomwe tikukonzeka kuyamba mwezi wa December lero tikambirana za matenda a Edzi. Dziko lonse lapansi limakumbukila za matenda a Edzi pa 1 December ndipo mutu wa chaka chino ndi," Tonse pamodzi titenge mbali popititsa patsogolo ntchito yolimbana ndi HIV"
Alendo athu achokera ku Blantyre District Health Office, ku Blantyre district council komanso ku National Aids Commission .
Tcherani wayilesi ya Times kuyambira nthawi ya 5:00 mpaka 6:00 madzulo kuti mumve zambiri.