Optivue Optometrists

Optivue Optometrists Your Family eyecare practitioner. We test eyes, fit Spectacles, contact lenses, low vision devices a

Big thanks to you guys  for all of your support! Mwabi Leaveson Thom, Memo Siyeni, Vladimir Sonke, Jim Patalia, Ekarhior...
28/11/2025

Big thanks to you guys for all of your support! Mwabi Leaveson Thom, Memo Siyeni, Vladimir Sonke, Jim Patalia, Ekarhiorhama Nayupe, Charls Chimalizen and .

And Congrats for being top fans on a streak πŸ”₯!

Enjoy your Friday πŸ’―!



Inu mwakonda iti? Samalani Maso anu posintha maonekedwe anu 😍.
26/11/2025

Inu mwakonda iti?

Samalani Maso anu posintha maonekedwe anu 😍.



Kumbikirani kuyedzesa Maso anu mzipatala zovomelezeka ndi a bungwe la Medical Council of Malawi kupewa kuononga Maso anu...
19/11/2025

Kumbikirani kuyedzesa Maso anu mzipatala zovomelezeka ndi a bungwe la Medical Council of Malawi kupewa kuononga Maso anu.

Pali zambiri zimene adokotala amayeza asanakupaseni magalasi ngati njira imodzi yothandizira mavuto osaona bwino.
Choncho musamangogula ma galasi paliponse musanayezedwe.



Zitetezeni Ku dzuwa ndi ma polarised sunglasses. Ziwanai kuti titha kupanganso mandala amene mmagwiritsa ntchito patali ...
20/10/2025

Zitetezeni Ku dzuwa ndi ma polarised sunglasses.

Ziwanai kuti titha kupanganso mandala amene mmagwiritsa ntchito patali kuoneka ngati awa ( prescriptive sunglasses).

Funsani kuti mumve zambiri.



Happy mother's day to you our valued clients!Abweleseni masteni tizawayeze Maso mwa ulele.
15/10/2025

Happy mother's day to you our valued clients!

Abweleseni masteni tizawayeze Maso mwa ulele.



Join us 😊!
12/10/2025

Join us 😊!

Kutentha uku kumafunika kuteteza maso anu Ku dzuwa.Pitani kwa a dokotala anu kuti mukayezese maso anu. Kondani Maso anu❀...
25/09/2025

Kutentha uku kumafunika kuteteza maso anu Ku dzuwa.

Pitani kwa a dokotala anu kuti mukayezese maso anu. Kondani Maso anu❀️.



Kumbukilani  kuyezetsa maso kamodzi  pa zaka ziwiri zilizonse ngati muli ndi zaka zoyambira 18 mpaka 65.Imbani 099629099...
20/08/2025

Kumbukilani kuyezetsa maso kamodzi pa zaka ziwiri zilizonse ngati muli ndi zaka zoyambira 18 mpaka 65.

Imbani 0996290997 kuti muziwe zambiri!



Mandala anu mmapukuta ndi chani akada?Gwiritsani ntchito zinthu zoyenelera kuti asakandike.Tili ndi madzi awa omwe ntchi...
22/07/2025

Mandala anu mmapukuta ndi chani akada?
Gwiritsani ntchito zinthu zoyenelera kuti asakandike.

Tili ndi madzi awa omwe ntchito yake ndikupukuta mandala anu.

Imbani 0899 441 975 or 0996 290 997 kuti muziwe zambiri.

Happy Independence day to you our valued clients.Our clinic will be open on Monday the 7th July from 8:30 to 13:00 hrs.E...
06/07/2025

Happy Independence day to you our valued clients.

Our clinic will be open on Monday the 7th July from 8:30 to 13:00 hrs.

Enjoy your holiday 😊!



Vacancy announcement!Optometrist (Full-Time)Optivue Optometrists (pvt) Limited invites suitably qualified and experience...
21/06/2025

Vacancy announcement!

Optometrist (Full-Time)

Optivue Optometrists (pvt) Limited invites suitably qualified and experienced personnel to apply for the position of optometrist based in Blantyre.

Qualifications sought are as follows:

β€’ BSc degree in Optometry from a recognized institution.
β€’ Licensed with medical council of Malawi
β€’ Two years working experience in Optometry practice
β€’ Driving license
β€’ Optometric Technicians (OTs) with relevant experience are encouraged to apply.

Key Responsibilities:

β€’ Performing all duties of an Optometrist
β€’ Managing day to day Operations for the practice
β€’ Developing strategic plans for the optometry practice
β€’ Conducting interviews and trainings for the new staff members
β€’ Making sure that the practice is registered with all regulatory bodies
β€’ Submitting daily, weekly and monthly reports to the managing director
β€’ Supervising stock taking process
β€’ Doing all duties as assigned by the Managing director/ Executive director

Kindly send updated CVs to optivueoptometrist@gmail.com no later than 27th June , 2025. State the expected salary range and benefits in your application.

Please note that only shortlisted candidates will be contacted.

Happy Father's day to all the Dads πŸŽ‰!Optivue Optometrists ili ndi magalasi oyenera  azibambo athu. Zawatengeleni madala ...
15/06/2025

Happy Father's day to all the Dads πŸŽ‰!

Optivue Optometrists ili ndi magalasi oyenera azibambo athu. Zawatengeleni madala mandala pa 20% discount.

Call/app +265 996 29 09 97 to book your appointment.



Address

VANMALI HOUSE P. O BOX 2339
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 13:00

Telephone

+265212519171

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Optivue Optometrists posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Optivue Optometrists:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram

Category