05/12/2025
Mangochi turn off
-Panopa tili pa Mangochi turn off township ya LIWONDE, posachedwa tikhala tikupita Ku LILONGWE* Malo oima Balaka, Nsipe, Ntcheu ndi Dedza
-Omwe muli ma derawa choonde sungani nthawi ndipo ngati muli busy, tumani munthu akhale ready chifukwa maderawa sitichedwamo pomwe takumana ndi omwe apereka order pompo pompo timakhala tikunyamuka
-Madongosolo ndi omwe aja Mukamanyamuka kuti mukufuna tikumane munene fukwa kulipo kufika kupeza tasuntha ndie sizimakhala bwino
-Ulendo timayenda chifukwa cha inu omwe munaberedwapo ndalama Ndipo mumati zachilengedwe herbals ithanso kukuberani, ndipo nthawi zambiri timakuuzani kuti *Ngati chikhulupiriro choti mukatumiza ndalama tikutumizirani ma herb anu mulibe choonde siyani musatumize ndalama yanu* izi timayankhula chifukwa timadziwa kuti nthawi zina timayenda ndipo m***a kugula pa manja
-Kodi munthu okuba angamayende mkumalengeza kuti tili dera lakuti lakuti? Apa tikupita Ku zochita mkumangotumiza ndalamazo tidzikakutumizirani aaaa
-Zachilengedwe herbals imatumizanso kunja Kwa dziko lino pa DHL ndi ma transporter ena monga Ku UK, America , Ireland, Qatar, South Africa, Tanzania, zambia ndi maiko ena..... Umboni pitani Ku Facebook aliko ma receipt ndi ma screenshot ake
Kodi nde ngati timatumiza Ku America nde zingavute mMalawi muno?
0886264833