Machiritso Natural Remedies

Machiritso Natural Remedies MACHIRITSO NATURAL REMEDIES! Please be advised that, Whatever we share here should not/Should never replace what the hospitals/Doctors tell you.

Mukadwala kapena Mukamva mthupi Thamangilani ku Chipatala!.

🇲🇼YOUR HEALTH IS OUR PRIORITY🇲🇼.

MAVUTO AWAMavuto a AsthmaMavuto a BPMavuto a SugarMavuto a pa khungu...Immune system...Mwaiona Remedy yake pogwiritsa nt...
28/04/2026

MAVUTO AWA
Mavuto a Asthma
Mavuto a BP
Mavuto a Sugar
Mavuto a pa khungu...
Immune system...

Mwaiona Remedy yake pogwiritsa ntchito Blackseed...Video yake ikubwela...

27/04/2026

EAR PAIN_HIGH BLOOD PRESSURE_BODAY PAIN

Ngati mukuvutika ndi High Blood pre...Makutu kuwawa...Thupi kuphwanya...ndi zina zambiri tamvani za Remedy iyi
__________________

26/04/2026

NGATI MUKUVUTIKA NDI MAVUTO AWA

Kuvutika mapumidwe,Kudzimbidwa, Kupanga mseru...

GOOD MORNING💥Mwadzuka bwanji lero................
26/04/2026

GOOD MORNING💥
Mwadzuka bwanji lero
................

READ THIS & SAVE ITChifukwa ndizofunikira  if you have;Headache- Eat BananaConstipated- Eat AppleSore throat - Eat Honey...
25/04/2026

READ THIS & SAVE IT
Chifukwa ndizofunikira if you have;

Headache- Eat Banana
Constipated- Eat Apple
Sore throat - Eat Honey
Toothache- Chew Clove
Tiredness- Eat Orange
Sleep issues- Eat Kiwi
Low blood sugar- Eat Dates
Bloating- Eat Yoghurt
Dry Hair - Eat Red Bell Pepper
Weak Memory- Drink Milk
Reduce Stress- Drink Green Tea
Dehydrated- Eat Cucumber
Glowing Skin- Eat Carrots
Improve Digestion- Eat Ginger
Boost Immunity- Eat Basil Leaves/garlic
Improve Eyesight- Eat Guava _Carrot

25/04/2026

GOOD MORNING Machiritso Natural Remedies FAMILY💥
Ndi bwino kuiwala zammbuyo ndikupanga focus pa tsogolo lanu...Have a Good Day

24/04/2026

🛑TSITSI KUTHOTHOKA🛑

Njira ya simple koma effective.
Ngati tsitsi likungothothoka tapangani izi:

Pezani Blackseed oil komanso coconut oil. Apangeni mix mafuta amenewa then mudzipanga massage mmutu mwanumo katatu pa week madzulo musanakagone. Mukapakamo zisiyeni usiku onse or tsukani after one hour ndi Shampoo wina aliyense wabwino okilinira tsitsilo /mild Shampoo.
Vuto lothothoka tsitsi mwathana nalo mudzingogwiritsa ntchito njira imeneyi.
_________________________
Osaiwala kuthandiza ena popanga LIKE...SHARE...

24/04/2026

Mupangeni tag Bestie wanu uja yemwe amati akakuona ukukangana ndi winawake amangofikira kulowelera even asakudziwa kuti chachitika mchani...pamapeto pake adzikufunsa KODI ZAKHALA BWANJI😀....

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Machiritso Natural Remedies posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share