DR KEN MW 1

DR KEN MW 1 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from DR KEN MW 1, Doctor, PLU, Lilongwe.

18/01/2023

Kunali family meeting kuntundu kwathu.ine chongoyelekedza kuima kuti ndiikilepo ndemanga ndangomva.zopempha ndalama zo kumapeto🙆‍♂️😰😰😰😰😰😰🙈🤷‍♂️

08/01/2023

Maybe 2023 might be your year to stop playing church and be church ,more dependence on God ,less disobedience more obedience.less worldly​ and more of God's word in you.cheers to slaying in christ.we have nothing (nothing )to boost in other than in Christ Jesus the true vine.

08/01/2023

Munakumana bwanji

Ken linali tsiku laku mulakho wa alhomwe nditafika pa amai ena ogulitsa katundu ndinasankha mikanda ya white nde nyamata anali side inayi atawona mikandayo anayankhula nati chemwa ineso mikanda imeneyo yandisangalatsa ine chongonena kuti ngati mungakwanitse kundigulila teloni, nyamata sanachedwa anatenga number yanga, nditafika kunyumba chama 10 usiku ndinalandila message yoti chemwali ngati mungapeze mpata tikumane ine Dr KEN sindinanyalanyaze ndinamuwuza kuti titha kukumana chifukwa kunena zowona naneso nyamatayo anandisangalatsa osati masewela, Ken nyamata anatumiza 40 thousand kwacha kuti ndiyendele ulendo wanga ochoka ku lilongwe kukafika ku mulanje ndikunena pano ndili ndi mimba yake nyamatayo ndipo pano tili limodzi

Dr KEN MW 1

07/01/2023

I don't know if this story fits for today but l need ur GMT to help me on how l can deal with the issue at hand

Dr ken, l have just found out that my boyfriend do ma******te and l just pretend like l did not see anything. Ndikapita kudeni kwake zimapezeka usiku around 2:00 Am wadzuka kumapanga zakezo ine ndili tulo and after that he sleeps kenako kudzukaso kupangaso. Ken imagine in a single night amapanga more than 5 times. Is this healthy abale? Chosecho ine ndimachitika kukakamiza kuti tipange deed, sadly, akayamba deed yo ndimachita kuthawapo ndekha-longlasting yakeyo🙌🙌

I have been dating him for a year now and am not tired but how best can l approach him on the issue so that he should stop as u know ma********on has its bad consequences. Is there medication to stop this? Now am with him koma ndachita kuthawa kuchipinda kuti ndiputidwe mphepo. Pliz GMT help.

-Shaaa! Kulakwa abale 😔 Madzi amchere aja katatu pa tsiku amathandizaso🤭GMT mukutipo bwanji?

07/01/2023

Hello DR KEN MW 1, hide my ID nane ndifotokoze my heartbreak story.

Ndinakhala pa relationship ndi mamuna wina wake for 2 years then anazapezeka kuti wachosedwa ntchito munthu nkufika pomasowa chakudya I was helping him kumpatsa money yogulira chakudya komanso yolipira rent because I was working then anazapezeka kuti wapezanso ntchito ina.

Kenako last year zinapezeka kuti wandipatsa mimba and anavomera kuti mimba ndi yake and kwa makolo anga anabwera ndi makolo ake kuzavomera mimba koma kuti tipange madongosolo kuti tikwatirane zinkaoneka kuti he was not ready to get married ndinangozisiya.

Koma DR KEN MW 1 mamuna anandionesa zinthu uyu mpamene ndinadziwa kuti kunja kuno kuli afiti amuna olo thandizo lili lonse osandipatsa zoti ati anthu amimba amanyengeleredwa ndi azimuna awo nkumafewa ine zimenezo sinazione ndipo kuvomera mimba nkusamapeleka support ndi chimodzi modzi kukana mimba.

Ndinachivomeleza I was just focusing on my unborn child ndipo ndinalibe maganizo otaya mimba coz ndinkati ndapeza best friend and indeed my unborn child was my best friend 🥰 ndinasamala ndekha mimba mpaka kufika nthawi yokapanga deliver unfortunately baby anapitilira may his soul rest in peace 😭😭😭😭

-Sorry for the loss annon 😔 MHSRIEP

DR KEN MW

TRUCK DRIVER WINA WAGULITSA THANKALA YONSE YAMAFUTA NDIKUTHAWAApolice ndi bungwe la Truck Drivers Association of Malawi ...
06/01/2023

TRUCK DRIVER WINA WAGULITSA THANKALA YONSE YAMAFUTA NDIKUTHAWA

Apolice ndi bungwe la Truck Drivers Association of Malawi TAM akusakasaka driver wina yemwe dzina lake ndi Emmanuel Mwamulowe pomuganizila kuti wagulitsa mafuta agalimoto onse omwe anali mu thankala yamafuta yomwe amachokela nayo ku Beira.

Mwamulowe atafika mudziko lino anagulitsa mafuta onse agalimoto pamtengo osika ndipo atapha ma million andalama anathawa mudziko lino osawonekaso komwe walowela

06/01/2023

S*x Is The Easiest Thing To Get These Days. S*x Is Everywhere. The Hardest Thing Is Love. Respect. Loyalty. Trust. Those Are Things You Can't Just Find. Anybody Can Have S*x With Anybody. There's Nothing Sacred About S*x Anymore. People Have S*x Before They Start Dating. People Have Children Before Marriage. S*x Has Become Easy. There Are Many Ways To Get It. You Don't Even Need To Think Hard. It's There For Everyone To Enjoy. Right Now Your Girlfriend Has Whatsapp. Facebook. Instagram. Twitter. Tik Tok. Snapchat. Out Of All These Platforms You Think You Are The Only Man She Talks To? Anybody Can Reach Her. Anybody Can Talk To Her. Some Guys She Won't Like. Some Guys Will Get Her Attention. Within That Process. Someone Will Score. There's No Way That She Can Be Rejecting Everyone Everyday. Someone Will Score. That's Why I Say S*x Has Become Meaningless. Find Someone With Loyalty. Respect. Kindness. Love & Care. Such Partners Are Rare -ambiri akutero

02/01/2023

Mutchuleni dzina ndipo mulangizeni

30/12/2022

Dear Men🧔 learn to forget
Money💸in your trousers 👖
It gives your woman a big
Motivation to wash your
Clothes 🥴😜

DR KEN MW 1 follow the page

30/12/2022

AFTER S*X WHAT NEXT.....MY DEAR IF YOU MISS THIS WRITE UP WHAT WILL YOU TELL YOUR FUTURE......

It's possible for any man to ask for s*x in a relationship, but is left for you as a lady to know that s*x, can't keep him..(S*x isn't enough)

There are two major factors ladies complain about s*x in a relationship:
√ After giving him my body he left me..
√ He left because I refused to have s*x with him..

NOTE: Both those who gave and those who refused to give are complaining...
( Whats the difference)

Ladies Listen, S*x isn't enough, its not the only thing you can offer a man.
If You Don't Have Anything To Offer A Man Outside S*x, Please remain Single...

A man can't stay with you because his having s*x with you....

Relationship is not buying and selling.
There are much to life than Monkey style, Doggy style, Missionary style, Apple n juice style, step pillows style, etc ...

Are you sound intellectually? Spiritually? Physically? Mentally? Emotionally?

Men love intelligent ladies...
Men love ladies with ideas..
Men love respectful ladies...
Men respect ladies that know what domestic work is
Men love and appreciate a woman who is good and excellent in multi-tasking
Men respect and honor ladies that wakes up very early in the morning to make sure that the kitchen is set.
Men respect ladies that keep their eyes at home than those that their eyes are always outside
Men love bravo ladies

S*x is very cheap these days, anybody can buy it.

You need to build yourself beyond s*x.
Leave make-ups and be a productive lady.
Men are looking for ladies with ideas and solution not those who paint their faces with different colours.

*What a man wants is beauty with brain not make ups with b***s or hips. Because all these will fail but what you have upstairs will remain.

Your husband complains because you think that you know it but you don't know it. Just do what your own husband wants and not what men want.

Tick tick to 2023 choose carefully desition define's destiny

30/12/2022

Nde kuli amuna ofuna nkazi ndamene aziwapembedza😪😤

Nawonso ma girls akati abweze ndipamene umadziwa kuti khobwe si nyembai zimangofanana nsunzi,,,,life yopembedzana inatha kale kale 😤

30/12/2022

Mu relationship yogonana dairy mukhoza kulimbamo kapena ai? 😎

Address

PLU
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DR KEN MW 1 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram

Category