Blessings Hospital

Blessings Hospital A Christian facility providing quality health care to the general public

We still have space in our general surgery camp next week!
02/10/2025

We still have space in our general surgery camp next week!

23/09/2025

Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m'bindikiro wochita ma opaleshoni osiyana siyana ndi madokotala ochokera ku America, kuyambira pa 4–10 October 2025 kwa sabata imodzi. Kuwunika ndi ndikuyika anthu pa m’ndandanda kuli mkati. Ndalama yowonera wodwara ndi MK1,000. Bwerani msanga pasanafike pa 4th October 2025 Madokotalawo ndi awa:
Wa Azimai (OBS & GYNAECOLOGY)
Adzachita ma opareshoni ngati awa:
Uchotsa zotupa za mchiberekero (fibroids Removal)
Uchotsa chiberekero ngati ndichowonongeka (HYSTERECTOMY)
Ndi zina
Dokotalayu adzaona anthu pa
Wa Onse (GENERAL SURGEON)
Adzachita ma opareshoni ngati awa
Hernia Repair
Uchotsa zotupa za pa khungu
Hydrocele repair
ndi zina
Dokotalayu adzaona anthu pa
Mtengo udzatengera opareshoni imene idzachitike uphatikizapo mankhwala, malo ogona ndi zina
Mitengo ikuyambira MK50,000 ulekeza MK300,000
Ma ward a private alipo pa Mtengo wowonjezera koma alipo ochepa, tilinso ndi EXECUTIVE WARD
Timalandiranso odwala ama medical insurance awa
MASM, MedHealth , Precious International, WEMAS/AIRTEL, Reserve Bank, National Bank LIHACO, To***co Commission, Gospel in Action ndi African vision Malawi
Mukafuna udziwa zambiri imbani phone pa 0994951443

A Christian facility providing quality health care to the general public

17/07/2025
Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m,bindikiro wochita ma o...
27/05/2025

Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m,bindikiro wochita ma opaleshoni osiyana siyana ndi madokotala ochokera ku America ndi ku Malawi, kuyambira pa 31ST May pakana pa 6th June 2025 kwa sabata imodzi. Kuwunika ndi ndikuyika anthu pa m’ndandanda kuli mkati. Bwerani msanga pasanafike pa 30th May 2025 Madokotalawo ndi awa:
Wa Onse (GENERAL SURGEON)
Adzachita ma opareshoni ngati awa
Hernia Repair
Uchotsa zotupa za pa khungu
Hydrocele repair
ndi zina
Dokotalayu adzaona anthu pa
Mtengo udzatengera opareshoni imene idzachitike uphatikizapo mankhwala, malo ogona ndi zina
Mitengo ikuyambira MK50,000 ulekeza MK300,000
Ma ward a private alipo pa Mtengo wowonjezera koma alipo ochepa, tilinso ndi EXECUTIVE WARD

Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m,bindikiro wochita ma o...
13/09/2024

Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m,bindikiro wochita ma opaleshoni osiyana siyana ndi madokotala ochokera ku America, kuyambira pa 05 – 11th October 2024 kwa sabata imodzi. Kuwunika ndi ndikuyika anthu pa m’ndandanda kuli mkati. Bwerani msanga pasanafike pa 4th October 2024 Madokotalawo ndi awa
Wa Azimai (OBS & GYNAECOLOGY):
adzachita ma opareshoni ngati awa, uchotsa zotupa za mchiberekero (fibroids removal), uchotsa chiberekero ngati ndichowonongeka (hysterectomy), ndi zina.
Wa Onse (GENERAL SURGEON):
adzachita ma opareshoni ngati awa, hernia repair, uchotsa zotupa za pa khungu, hydrocele repair, ndi zina.
Dokotalayu adzaona anthu pa
6th October 2024, 1 pm.
Mtengo udzatengera opareshoni imene idzachitike uphatikizapo mankhwala, malo ogona ndi zina
Mitengo ikuyambira MK30,000 ulekeza MK200,000
Ma ward a private alipo pa Mtengo wowonjezera koma alipo ochepa.

15/07/2024

Medical council of Malawi yavomereza chipatala cha Blessings ku Lumbadzi, kuti chikhoza kuchita m.bindikiro sochita ma opaleshoni osiyana siyana ndi madokotala ochokera ku America, kuyambira pa 20-26 July 2024 kwa sabata imodzi. Kuwunika ndi ndikuyika anthu pa m'ndandanda kuli
mkati. Bwerani msanga pasanafike pa 20 July 2024. Madokotalawo ndi awa:

Wa Azimai (OBS & GYNAECOLOGY)|
Adzachita ma opareshoni ngati awa:
Uchotsa zotupa za mchiberekero
(fibroids Removal)
• Uchotsa chiberekero ngati
ndichowonongeka (HYSTERECTOMY)
• Ndi zina

Wa Onse (GENERAL SURGEON)
Adzachita ma opareshoni ngati awa
Hernia Repair
- Uchotsa zotupa za pa khungu
• Hydrocele repair
ndi zina

Dokotalayu adzaona anthu pa
20 July 2024, 8:00 am

Mtengo udzatengera opareshoni imene idzachitike uphatikizapo mankhwala, malo ogona ndi zina
Mitengo ikuyambira MK25,000 ulekeza MK150,000
Ma ward a private alipo pa Mtengo wowonjezera koma alipo ochepa.

Mukafuna udziwa zambiri imbani phone pa 0994951443.

A Christian facility providing quality health care to the general public

04/07/2024

A Christian facility providing quality health care to the general public

22/07/2023

Ku Chipatala cha Blessings ku Lumbadzi kwabwera madokotala ndi manurse ochokera ku America kudzachita ma operation kuyambira pa 22 July 2023 kwa sabata imodzi. Dokotala m'modzi wa amai adzapanga ma operation ochotsa zotupa za mmimba, fistula repair, ndi zina, wa azibambo ndi amayi odzachita ma general operations ngati hernia, zotupa za pakhungu, ndi zina. A medical officer ndi clinical officers adzaonana ndi wodwala asanaonane ndi ma dokotala. Mtengo wolembetsera ndi K800. Opaleshoni ina iliyonse ili ndi mtengo wake koma wokuthandizani. Bwerani msanga kudzaonedwa ndi madotolo athu apa chipatala chino kuti adzakuikeni pa ndandanda wodzaonana ndi madokotala akubwerawa. Imbani phone pa 099 495 1443 ndi WhatsApp 0999394327 kuti mudziwe zambiri, kapena tumizani email ku info@blessingshospital.com. Timapezeka pa M1 ku mpoto kwa Kamuzu International airport main turnoff. Timalandira ma membala a MASM, MedHealth, Precious Medical International, To***co Control Commission, LIHACO, Malawi catering service Limited, Reserve Bank ndi Landirani Trust. Zikomo Ambuye akaudalitseni.

Address

P. O. Box 146 Lumbadzi
Lilongwe

Opening Hours

Monday 00:00 - 23:59
Tuesday 00:00 - 23:59
Wednesday 00:00 - 23:59
Thursday 00:00 - 23:59
Friday 00:00 - 23:59
Saturday 00:00 - 23:59
Sunday 00:00 - 23:59

Telephone

+265999394327

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Blessings Hospital posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Blessings Hospital:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram

Category