Care MW

Care MW careMW󱢏
"Timaphunzitsa kapewedwe ka matenda osiyanasiyana.
(4)

Mwaulele,muli kunyumba kwanu"
" ONCE YOU SEE THIS FOLLOW THE PAGE"
"INVANI ZOONA ZOKHUZA KUCHIPATALA "
"KUCHIMAKE KWA UPHUNGU WAKUCHIPATALA "
👉caremw217@gmail.com.WhatsAp0999376652

04/02/2026

Kumawatenga achikondi anu koyezesa inu muchedwa pati team chipatala 😧

゚viralシfypシ゚ ゚viralシfypシ゚viralシalシ

st yosefe college of health science with their beautiful nurses 🥳
04/02/2026

st yosefe college of health science with their beautiful nurses 🥳

04/02/2026

Nde uzisegula mmimba uli ndi chimfine 🙄🙌

04/02/2026

Care MW 2.0 󱢏 🔥

04/02/2026

Normal Blood presure
Pafupifupi 120/80 mmHg.
*90-100 systolic.
*60-90 diastolic
Hypertension imakhala pamene magazi ali 140/90 mmHg kapena kuposa.

A.Zimayambitsa / Zoika pachiwopsezo:
✓Kudya mchere wambiri
✓Kunenepa kwambiri
✓Kusachita masewera olimbitsa thupi
✓Kusuta ndi kumwa mowa
✓Nkhawa (stress)
✓Mbiri ya m’banja
✓Matenda ena monga matenda a impso.

Zizindikiro:
Nthawi zambiri palibe zizindikiro, koma ena amatha kukhala ndi:
✓Mutu kupweteka.
✓Maso kusawona bwino.
✓Kupweteka pachifuwa.
✓Kupuma movutika.
Zovuta zake:
✓Stroke
✓Matenda a mtima
✓Kulephera kwa impso
✓Vuto la maso.

Kupewa ndi kuwongolera:
✔ Chepetsani mchere
✔ Muzichita masewera
✔ Sungani thupi lolemera moyenera
✔ Lekani kusuta
✔ Chepetsani mowa

Masana abwino team chipatala🔥💪🏥
04/02/2026

Masana abwino team chipatala🔥💪🏥

pankhani ya kuuka kwa akufa ija ,inu munthu uyu mutamupeza malangizo omwe mungapase ndi Oti Chan kutengela ndi mene amal...
04/02/2026

pankhani ya kuuka kwa akufa ija ,inu munthu uyu mutamupeza malangizo omwe mungapase ndi Oti Chan kutengela ndi mene amalankhulira muja 😧?

Mawu Ake a mukanema uja anati "Wowing'iiiiiiiiiiiiiiii😧,fumuuuu, aishing'iiiiiiiii yumiiii I love you geshiooootooo isiyee💀

Good morning team chipatala 🌄
04/02/2026

Good morning team chipatala 🌄

akuti zoyendera no🙅👇*Government Orders Council Officers to Reside in Their Duty Districts*The Ministry of Local Governme...
03/02/2026

akuti zoyendera no🙅👇

*Government Orders Council Officers to Reside in Their Duty Districts*

The Ministry of Local Government and Rural Development has directed all council officers to reside in the districts where their designated duty stations are located, citing growing concerns over absenteeism and inefficiency caused by long-distance commuting.

In a circular signed by Secretary for Local Government and Rural Development, Rev. Moses Owen Chimphepo, the Ministry observed that several officers were living in cities or districts other than their official duty stations, a situation that has led to late reporting for duty, increased absenteeism, and misuse of council resources such as fuel.

“The practice undermines efficiency, accountability, and the quality of public service delivery at the local council level,” reads part of the statement.

The directive, which takes immediate effect, requires all affected officers to relocate and take up residence within their duty districts, in line with applicable public service regulations

chonde asakubeleni izi nza fake vacancy yama HSA sinatuluke
03/02/2026

chonde asakubeleni izi nza fake vacancy yama HSA sinatuluke

03/02/2026

Ambiri mwatipanga tag kuti achipatala mukutipo bwanj 💀 yankho ndiloti nkhan zaku mudimazi nafe simbali yathu 😧

゚viralシfypシ゚ ゚viralシfypシ゚viralシalシ

Address

Area
Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Care MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Care MW:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram