Mankhwala amchilengedwe Hoceda rsps

  • Home
  • Mankhwala amchilengedwe Hoceda rsps

Mankhwala amchilengedwe Hoceda rsps Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mankhwala amchilengedwe Hoceda rsps, Medicina e saúde, .

*Thesani vuto losowa magazi lero*Tikuluza achibale ambili kamba kosowa magazi nde lero aphiri abwera kuzaulula zinsinsi ...
09/12/2024

*Thesani vuto losowa magazi lero*
Tikuluza achibale ambili kamba kosowa magazi nde lero aphiri abwera kuzaulula zinsinsi zozama za mmene tingathesere vutoli
Chifukwa cha kuchuluka zochita sindikukwanisa kulemba nkhani tsiku ndi tsiku koma musachoke mgulu lino chifukwa apo ndi apo zabwino zizibwera

Mankhwala amphanvu othesera kusowa kwa magazi ndi masamba cabichi kupanga tiyi osakaniza ndi tsabola
Koma ngati mukufuna zachangu kwanbili pezani kalombo komwe pachiputukezi timati catato
Kalomboka sindidziwa kuti mu chilankhulo chanu mumati chani koma ndikuonesani chithunzi
Nde mukufunika kusinja kupanga ufa mkumamwa ngati tiyi ufawo olo kungophika mkumupasa adye odwalayo
Pa masiku atatu okha odwala apeza magazi onse omwe thupi lake likufunikira
Si zokhazo mukapangira odwala matenda ashuga mphanvu ya catato ndi yofanana ndi mapilisi otchedwa metiformin aja amene amakankha shuga kuchosa mmagazi kulowesa mmaselo athupi zikatero munthu amapeza bwino koma vuto la metiformin ndi loti amatsitsa mphanvu za kubedi mpamene catato amaonjeza mphanvu mwa odwala .pali zambili zoti ndikuphunziseni za katato koma mpata ndi ochepa ndizilemba pamgonopamgono chomwe mukufunika kudziwa ndi choti pali catato yemwe amagwa mmakungwa a mtengo woola komanso pali zija zimagwa mmasamba zonse ntchito ndi yofanana
Katato ali ndi ma protein ambili kuposa msomba komanso kuposa nyama ya mgombe katato ali ndi chilichonse chothandiza kuti munthu akhale moyo.

30/06/2024

ndinapempha kuti mutithandizeko kupeza ka shop mu lilongwe ndi mu blantyre titsegule shop yathu ya ma herbs koma kuli ziiii

mumadziwapo chiti apapa,ndemanga zanu ndimaziyamikira,tchulani dzina la mtengo ulionse paokha tione ngati mumazidziwa, n...
26/09/2023

mumadziwapo chiti apapa,ndemanga zanu ndimaziyamikira,tchulani dzina la mtengo ulionse paokha tione ngati mumazidziwa, ndemanga zikakwana 100 mpomwe ndifotokoze za ntchito ya mitengoyi

19/09/2023

*mchifukwa chiyani ndimanya zonunkha kwambili?*
nkhani ili mmatumbo
mmatumbo muli mphanvu yotchedwa pepsin
mlhanvuyi imagaya ma protein athu koma ikasokonekera mkulephera kugaya ma protein ma proteiniwo amalowa mmatumbo ndipo amakasanduka poizoni yotchedwa cadaverine
zomwezi mzomwe zimanunkhisa kwambili manyi yathu nde ngati mumanya zonunkha kwambili dziwani kuti mukutaya zofunika kuchimbudzi,ma protein safunika kutaidwa ndipo kunyunkha kwa tuvi kuzikhala kwa bola osati kukhala ngati mwanya mbuzi yoola aaaa inuuuuuu zimaonjeza pena muzizidera nkhawa mukamaona chinachake chosakhala bwino chikuchitika mthupi mwanumo,ndapita mukandifuna kuti ndikuphunziseni zambili mkalasi mwanga mundipeza kuseliku,ndikujambula ma video ya maphunziro a online kwa ofuna kuphunzira

18/09/2023

kodi muli ndi vuto lonenepa kwambili makungwa ya zipatso za galagadeya amathesa vutoli chimachitika ndi choti mmakungwamu muli mamkhwala otchedwa pectin mankhwalawa akalowa mthupi amamwa mafuta onse a mthupi nde chinthu china ndi choti thupi lathu silikwanisa kugwilisa ntchito pectin ameneyu nde ngati thupi siliyamwa pectin ndiye kuti amatuluka kuchimbudzi nde mukuona bwanji iye wamwa mafuta koma thupi likumutulusa kodi asiya mafuta wamwa aja?pectin ndi mbavatu imaba mafuta mkutuluka nawo kunja,imwayi tiyi wa ufa wa makungwa ya galagadeya muthese mafuta mthupi maka inu oneneka kapena inu muli ndi mimba zazikulu

18/09/2023

mukufuna kusiya kusuta kapena kumwa mowa koma zikukanika?lero mudziwa mtengo wamphanvu kwambili pa vutoli

ngakhale aja mahule oti amafuna atasiya uhule koma zikuvuta mtengowu umathandiza

choyamba dziwani kuti chizolowezi chimakhazikika mu mtima mukapanga chinthucho kwa masiku 21 otsatizana
nde ngati mukufuna kusiya chinthucho mukufunika kumwanso mankhwalawa kwa masiku 21 otsatizana
ndinanena nthawi zonse kuti mankhwala amphanvu saavuta kupezeka ingopezani masamba ya galagadeya muwilise mumwe kapu imodzi katatu pa tsiku muzasiya chizolowezi chilichonse pa thupi lanu
chenjezo mukafuna kugwilisa ntchito masamba ya galagadeya muziwilisa masambawa chifukwa ali ndi mankhwala otchedwa
cyanogenic glycoside
mamkhwalawa akalowa mthupi mwa munthu amasanduka mankhwala otchedwa hydrocyanic acid
mamkhwalawa amayambisa matenda otchedwa cyanosis ndipo amapha
ena mwa mitengo ali ndi mankhwala oupa chonchi ndi chinangwa🫢 aaa aphiri ifetu timakukuta chinangwa koma sitifa bwanji? oohhh simufa koma mumafa kabisila matenda mukudwala aja mukudziwa kuti anachokera pati?mtengo wina uli ndi poizoniyi ndi nthanga za apozi ngati mukufuna kufa yesani lero lomwe lino musinje nthanga za apozi mumwe muone ngati mawa mudzuka wamoyo
chinangwa mukachidya chachiwisi chikakanika kukuphani chimathamangisa ku ziwalo zoberekera kenako zimaotcha inu mkumanva ngati mphanvu zaonjezeka za kubedi,kumeza nthanga ya apozi kulibe vuto chifukwa ndulu siikwanisa kusinja nthanga ndipo mukaitulusa kuchimbudzi koma kuisinja mkumwa mwamwa poizoni basi

nde mankhwala ndi oipa koma amatha kuchosedwa.motani?wilisani masamba ya galagadeya kapena phikani chinangwa mukatero mumakhala kuti mwachosa poizoni yonse yoipa
chinangwa ngakhale kungochisinja mamkhwalawa amatha kuchoka posinja chifukwa mphanvu yake yoipayo ndi yochepa kwambili
masamba ya galagadeya kupatula pa kuthesa chizolowezi yamathesa matenda amaganizo komanso kusowa tulo si zokhazo mankhwalawa amathesa khunyu ngati mumasowa tulo,muli ndi khunyu,muli ndi chizolowezi kapena mphanvu kubedi ndi zotsika imwani masamba ya galagadeya

23/06/2023

Nao perca grande promocao dos nossos produtos na farmacia hoceda enquanto aguardamos o dia 15 de julho chegue para abrir a maior farmacia de plantas medicinais em Moçambique aqui mesmo na cidade de TETE
DE DIA 25 DE JUNHO A DIA 14 DE JULHO TERÁ DESCONTO DE 20%
E NO DIA DE ABERTURA QUE SERÁ DIA 15 DE JULHO DESCONTO ATÉ 50% SO VALIDO DIA 15

Address


2300

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mankhwala amchilengedwe Hoceda rsps posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

  • Want your practice to be the top-listed Clinic?

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram