30/10/2021
*KUTSUKA M'THUPI*
NJIRA YOPHWEKA KWAMBILI,
👉 Njira iyi ngakhale mamuna kaya akufuna kutsuka m'mimba atha kugwirisa ntchito.
*👉 "Kwainu azimayi kuti kulera achoke mwansanga igwiritseni ntchito njira iyiyi ndipo idzakuthandizani kwambili👇."*
👉 Paliso anthu ena m'mimba mwawo👇
– Mumangolira phokoso lachilendo komanso kumangokhala yokhuta,
*"Njira yake ndimeneyi👇 yothana ndimavuto ose tanena pamwambawa.*
👉 Pezani sugar ma teaspoons 8.
👉 Pezani Alovera wanthete masamba atatu or awiri.
👉 Mumusinje bwino Alovera yo apange phala phala,
&
– Ikani mu botolo la 1 liter, thiranimo ma teaspoons 8 a Sugar.
– Khutchumulani botolo lo mutalitseka kukamwa.
– Mulikhutchumule kwa mphindi zisanu kuti zisakanikirane bwino.
– Nde mudikire kwa maora awiri nde mudzamwe zonsezo.
– Ndiyachangu njira imeneyi.
– Pangani zimene kawiri pa week, mudzabadwaso mwatsopano ngati mnamwari komanso bambo mnyumbamo sadzadandaula kuti akufooka,
Mwakoma nonse